Mawu a M'munsi
b Magazini ya Galamukani! siilangiza anthu za chithandizo chowayenerera, za mankhwala amene ayenera kumwa kapenanso opaleshoni imene ayenera kuchitidwa. Wodwala aliyense ali ndi udindo wofufuza yekha ndi kulingalirapo bwino pa za njira iliyonse imene angagwiritse ntchito kuti achire malingana ndi mmene akuidziƔira.