Mawu a M'munsi
a Munthu aliyense amadya zimene amakonda. Magazini ya Galamukani! siikunena kuti muyenera kudya kapena kusadya zakudya zosiyanasiyana zimene zatchulidwa m’nkhaniyi, chifukwa chakuti anazikonza pogwiritsa ntchito njira zinazake. Nkhanizi zalembedwa n’cholinga chofuna kudziŵitsa oŵerenga mfundo zimene zikudziŵika panopa.