Mawu a M'munsi
b Mawu a m’Chigiriki onena kuti dama ndi por·neiʹa. Mawuŵa amatanthauza khalidwe lina lililonse lokhudza nkhani ya kugonana pogwiritsa ntchito maliseche musanakwatire. Zimenezi zingaphatikizepo kugwiranagwirana kumaliseche pofuna kudzutsirana chilakolako chogonana ndiponso kugonana mkamwa.