Mawu a M'munsi
a M’nkhani zino, tikanena za anthu amene awaumiriza kuchoka kwawo, sitikunena za anthu oyambira pa 90 mpaka 100 miliyoni amene amawaumiriza kuti achoke m’nyumba zawo pofuna kutukula deralo monga kumanga madamu, kukumba migodi, kudzala mitengo kapena kuchita ntchito zina zaulimi.