Mawu a M'munsi
a Malinga ndi zimene akatswiri anafufuza zikusonyeza kuti anthu akapita padera zimawakhudza mosiyanasiyana. Anthu ena mutu wawo sugwira, ena amataya mtima, komanso ena amachita chisoni kwambiri. Ofufuza amati kulira n’kwachibadwa ndipo kumathandiza munthu kuiwala msanga pakachitika vuto linalake, monga kupita padera.