Mawu a M'munsi
b Kaonaneni ndi dokotala wanu kuti akuuzeni kuchuluka kwa mchere umene muyenera kudya ngati mukudwala matenda a kuthamanga kwa magazi kapena mtima, chiwindi, kapenanso impso ngati mukulandira mankhwala.