Mawu a M'munsi
a Komabe kungoona kuchuluka kwa mabanja, makamaka kwa padziko lonse, kukhoza kutinamiza. M’madera ambiri, muli mabanja amene ndalama zawo sizinachuluke n’komwe m’kati mwazaka 50 zapitazi, koma malipiro a anthu ena m’maderawo achita kuŵirikiza kangapo.