Mawu a M'munsi
a Gululi, limene lili ndi atsogoleri 28 otchuka padziko lonse, linalemba lipoti lalitali m’chaka cha 1995 la mutu wakuti, “Mgwirizano Wathu Padziko Lonse,” ndipo mu lipotilo analembamo zimene akuganiza kuti maboma apadziko lonse asinthe n’cholinga choti aziyendetsa bwino zinthu.