Mawu a M'munsi
c Popeza kuti masiku ano anthu ena amagonera limodzi kuti azichita zosayenera, nkhani ino ikukamba za akazi okhaokha kapena amuna okhaokha amene amakhala nyumba imodzi kuti azithandizana pankhani ya ndalama komanso pazinthu zina zofunika.