Mawu a M'munsi
a M’zaka 100 zoyambirira za m’nyengo yathu ino, anthu ankakonda kudya kapena kumwa kwambiri pamapwando aakuluakulu achiroma. Choncho, Akristu ankachenjezedwa kuti asalole kuti zakudya kapena zina zilizonse zotere ziwasandutse akapolo.—Aroma 6:16; 1 Akorinto 6:12, 13; Tito 2:3.