Mawu a M'munsi
a Galamukani! siilangiza anthu za chithandizo chilichonse cha mankhwala. Malingaliro amene alembedwa m’nkhani ino okhudza akazi kapena amuna sangagwire ntchito kwa aliyense, ndipo mfundo zina mwina sizingagwire ntchito n’komwe kwa ena.