Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Chifukwa chakuti mwezi ndi dziko zimadutsa m’njira zozungulira ngati dzira, kukula kwa dzuŵa ndi mwezi kumasinthako pang’ono malinga ndi malo omwe zili m’njira zawozo. Mwezi ukapita kutali kwambiri ndi dziko, chigawo cha mdima kwambiri cha mthunzi wake sichingafike padziko pano. Zikatere, m’madera omwe mwadutsa mthunziwo padziko lapansi pano mumachitika kadamsana yemwe dzuŵa limaphimbika pakati, ndipo limaoneka ngati mphete yonyezimira itazungulira chinthu chakuda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena