Mawu a M'munsi
a Pochita mayere, ankatenga tinthu ting’onoting’ono monga timiyala kapena timitengo n’kutikulunga m’chovala kapena kutiika m’chikho. Kenaka ankatipukusa zolimba. Ndiyeno ankatolapo kanthu kamodzi ndipo mwini wa kanthuko ndiye amene ankamusankha.