Mawu a M'munsi
a Akatswiri a zachikhalidwe cha anthu amanena kuti azimayi olera ana popanda bambo alipo ochuluka mochititsa nthumanzi poyerekezera ndi azibambo otere.’ Motero, mbali yaikulu ya nkhanizi ikukhudza makamaka azimayi. Komabe mfundo zimene zakambidwamo n’zogwiranso ntchito kwa azibambo.