Mawu a M'munsi
a Constantine pamodzi ndi mayi ake a Helena ankafunitsitsa kudziƔa malo opatulika a ku Yerusalemu ndipo mayi akewo anapitako. Kungoyambira pamenepo anthu enanso ambiri anali kuchitabe chimodzimodzi kwa zaka zambirimbiri.