Mawu a M'munsi
c Kulankhulana kapena kulemberana mauthenga kaŵirikaŵiri patelefoni ndi munthu amene si mwamuna kapena mkazi mnzanu ndi njira ina yochitira chibwenzi. Onani nkhani yakuti “Achinyamata Akufunsa Kuti—Kodi Cholakwika N’chiyani ndi Kulankhulana?” mu Galamukani! ya September 8, 1992.