Mawu a M'munsi
a Mankhwala otere amawapanga motsanzira mankhwala amene makampani ena opanga mankhwala amapanga. Mayiko amene ali m’Bungwe Loona Zamalonda la Padziko Lonse amaloledwa mwalamulo kupanga mankhwala a makampani enaake pakachitika zinthu zamwadzidzidzi.