Mawu a M'munsi
a Mizinda ya New York, Los Angeles ndiponso Chicago ili ndi anthu ochulukirapo poyerekeza ndi a mumzindawu. Anthu amene amakhala mumzindawu alipo pafupifupi 3,500,000 ndipo mzindawu ndi wochepa pang’ono poyerekeza ndi dziko la Swaziland.