Mawu a M'munsi
a Zombozi n’zosiyanasiyana kukula ndiponso kapangidwe kake, malingana ndi kumene zimayendako, kaya n’kumadoko, panyanja, kapena kumadera a kumtunda ndi kumunsi kwa dziko lapansili. M’nkhani ino tikukamba makamaka za zombo zimene zimayenda panyanja.