Mawu a M'munsi
a Zina mwa zakudya zimene zili ndi mavitamini olimbitsa mafupa ndiponso owonjezera magazi ndi chiwindi, ndiwo za m’gulu la nyemba, ndiwo za masamba, mtedza, ndiponso phala lotendera. Kuti thupi ligaye bwino zakudya za mavitamini owonjezera magazi ndi bwino kudyanso zipatso.