Mawu a M'munsi
b Mayi amene watenga pathupi ali wathanzi amafunika kuti panthaŵi yochira akhale atawonjezera makilogalamu 9 kapena 12. Komabe, atsikana aang’onoang’ono kapena amayi omwe ali ndi vuto la kupereŵera kwa zakudya m’thupi ayenera kuwonjezera makilogalamu 12 kapena 15, pamene amayi omwe ndi onenepa kwambiri ayenera kuwonjezera makilogalamu 7 kapena 9 basi.