Mawu a M'munsi
a Emil Jellinek, amene anapereka ndalama zambiri zoyendetsera kampani ya Daimler, anaganiza zoti galimoto zatsopanozo azizitcha dzina la mwana wake wamkazi, Mercedes. Iye ankaopa kuti galimoto za dzina la Chijeremani lakuti Daimler sizingakayende malonda ku France.