Mawu a M'munsi
b Poyamba galimotozi ankazigulitsa pa mtengo wa madola 850 koma podzafika m’chaka cha 1924 galimoto yongopangidwa kumene ya mtundu wa Ford ankaigulitsa pa mtengo wotsika kwambiri wa madola 260 okha basi. Anapitiriza kupanga galimoto za mtundu wa Model T kwa zaka 19, ndipo m’zaka zimenezi anapanga galimoto zoposa 15 miliyoni.