Mawu a M'munsi
b Munthuyo amagona kumaso kwake atavalako chinthu chotulukira mpweya wochokera m’makinaŵa n’kudzera m’paipi yotha kupindikira mbali iliyonse. Mpweya umenewu umathandiza kuti munthuyo asabanike ndiponso kuti azipuma bwinobwino.