Mawu a M'munsi
a Nthochi zikamapsa zokha, zimatulutsa mpweya woterewu umene umapangitsa kuti zipse msanga. Apa ndiye kuti njira ina yoti nthochi zosapsa zipse ndiyo kuziika pamodzi ndi nthochi zingapo zakupsa.