Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, n’zotheka kuti ena amene ankalambira mafano asanakhale Akristu sankatha kusiyanitsa kudya nyama ndi kuchita zinthu zokhudzana n’kulambira. Chifukwa china chomveka n’chakuti Akristu osakhwima chikhulupiriro akanatha kuiona nkhaniyi molakwika n’kukhumudwa.