Mawu a M'munsi
a NthaƔi zambiri akazi amene amapezerera anzawo amagwiritsa ntchito njira monga, kusacheza ndi anthu amene amawapezererawo ndiponso kufalitsa mphekesera zonyansa. Komabe zikuoneka kuti ambiri ayamba kuchitanso zachiwawa.