Mawu a M'munsi
a Nthaŵi zambiri anthu ovala zovala za pa zionetsero za mafashoni amafunika kukhala “aatali mosachepera mamita 1.74, ochepa thupi kwambiri, okhuthala milomo, a masaya otukuka, a maso aakulu bwino, a miyendo yaitali ndiponso a mphuno yowongoka koma osati yaikulu kwambiri,” inatero magazini ya Time.