Mawu a M'munsi
b Bungwe la ku United States loona za mavuto otere lotchedwa National Association of Anorexia Nervosa and Associated Disorders linati anthu pafupifupi 8 miliyoni ali ndi vutoli ku United States kokha ndipo linati ambiri ndithu amafa nalo kumene. Ambiri mwa ameneŵa (86 pa 100 alionse) anayamba kukhala ndi mavuto okhudza kudya asanakwanitse zaka 21.