Mawu a M'munsi
a Nthaŵi zina mafuta a pansi panthaka amatulukira pamtunda kudzera m’ming’alu. Kuwonjezera pa kukhala amadzimadzi, mafutaŵa amapezekanso mumpangidwe wonga tala, kapena phula.