Mawu a M'munsi
a Galamukani! si magazini ya zachipatala ndipo siuza anthu mankhwala owayenerera kapena chakudya choti azidya, kaya akhale mankhwala ochokera ku zitsamba kapena ayi. Zimene muŵerenge mu nkhani ino n’zokudziŵitsani zina ndi zina zofunikira basi. Oŵerenga ayenera kusankha okha zimene angatsate pankhani yokhudza thanzi lawo ndi mankhwala amene akufuna.