Mawu a M'munsi
a Dziŵani kuti zizindikiro zina zotere zimasonyeza kuti munthu akuchita misala, akugwiritsira ntchito mankhwala osokoneza bongo, kapena zingakhalenso zimene zimachitika mwachibadwa wachinyamata akamakula. Munthu angadziŵike kuti alidi ndi matenda ameneŵa pokhapokha ataonedwa bwinobwino ndi dokotala wodziŵa bwino za matendaŵa.