Mawu a M'munsi
a Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures, limene limafalitsidwa ndi Mboni za Yehova, ndi Baibulo limene linamasuliridwa mwamakono ndiponso mawu ake amagwirizana ndi mmene anthu amayankhulira panopo. Chinthu chofunika kwambiri m’Baibulo limeneli n’chakuti linabwezeretsa dzina la Mulungu pena paliponse pamene linayenera kukhalapo m’Malemba a Baibulo. Panopa, mabaibulo ameneŵa, athunthu kapena mbali yake yokha, oposa 122 miliyoni asindikizidwa m’zinenero zokwanira 45.