Mawu a M'munsi
a Nkonono wodukizadukiza komanso wosokosa wa matenda obanika kutulo n’ngosiyana ndi nkonono umene anthu ambiri amachita mwa apo ndi apo, umene umangomvekera chapansipansi, womwe kuipa kwake n’koti ngati muli anthu ena m’chipindamo amalephera kugona.