Mawu a M'munsi
b Kuti mudziŵe mfundo zina zimene zingakuthandizeni kugonjetsa vuto loseŵeretsa maliseche pofuna kudzisangalatsa, onani buku lakuti Achichepere Akufunsa—Mayankho Amene Amathandiza, masamba 198 mpaka 211, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.