Mawu a M'munsi
a Malingana ndi cholinga chake, magazini ya Galamukani! ‘siloŵerera m’ndale.’ Cholinga cha nkhani ya kusintha zinthuyi ndicho kungowadziŵitsa aŵerengi athu za nkhaniyi ndiponso kuwasonyeza njira yokhayo yomwe ingathetsedi mavuto athu anthufe.