Mawu a M'munsi
b Zimene anapeza atafufuza zimaonetsa kuti ambiri mwa anthu amene amavutitsidwa kuntchito ndi akazi, komabe n’zotheka kuti mwina n’chifukwa choti akazi ndiwo amakonda kunena za vutoli ndiponso kufuna thandizo.