Mawu a M'munsi
a Nthomba inali nthenda yabwino kuithetsa kudzera mu katemera wapadziko lonse chifukwa chakuti, mosiyana ndi matenda amene amafalitsidwa ndi zamoyo zina zovutitsa monga makoswe ndi tizilombo towuluka, kachilombo koyambitsa nthomba kamadalira munthu kuti kapulumuke.
[Chithunzi]
Mnyamata wa ku Ethiopia akulandira katemera wa poliyo wodonthezera m’kamwa
[Mawu a Chithunzi]
© WHO/P. Virot