Mawu a M'munsi
a Chilamulo cha Mose chinali ndi malangizo okhudza katayidwe ka zonyansa, ukhondo, ndi kuika odwala kwaokha. Dr. H. O. Philips anafotokoza kuti “nkhani zokhudza kubereka, kutulukira matenda, kuchiza matenda, ndiponso khalidwe loteteza ku matenda zimene zili m’Baibulo n’zotsogola ndi zodalirika kwambiri kuposa zimene ankaphunzitsa Hippocrates.”