Mawu a M'munsi
b Nkhani ino ikukhudza anthu amene amalankhulidwa mawu opweteka kapena amamenyedwa. Malangizo amene angathandize anthu amene amachitira anzawo zinthu zimenezi anaperekedwa mu nkhani zakuti “Kuleka Mawu Opweteka ndi Kunena Mawu Olamitsa” ndi “Kuchita Mfunzi—Kodi Kumavulaza Motani?” mu magazini yathu ya November 8, 1996, ndi ya April 8, 1997.