Mawu a M'munsi
a Mastadiya anali muyezo wachigiriki woyezera kutalika kwa chinthu. Ngakhale kuti kukula kwake kunkasiyanasiyana m’madera osiyanasiyananso, zikukhala ngati stadiya imodzi inkakhala yaitali mamita 160 mpaka 185.