Mawu a M'munsi
b Ngakhale kuti amuna ndi akazi omwe angathe kulankhulidwa mawu opweteka kapena kumenyedwa, bungwe la U.S. Centers for Disease Control and Prevention linati “akazi ndi amene amapwetekedwa kwambiri kuposa amuna.” Choncho, pofuna kufeŵetsa zinthu, mu nkhani ino tizilankhula ngati munthu wozunzayo ndi mwamuna.