Mawu a M'munsi
e PanthaƔi zina, mwachitsanzo ngati mwamunayo amafuna kukugwirirani, makolo anu angafune kuti akanene zimenezo kupolisi. Kuchita zimenezi kungachititse kuti atsikana ena asadzakumanenso ndi zoopsa ngati zimene mwakumana nazozo.