Mawu a M'munsi
a Mphaka wa ku Spain ameneyu anamuika pa gulu la nyama zimene “zili pangozi yaikulu” mu chikalata chotchedwa Red List, chimene amalembapo nyama zimene zatsala pang’ono kutha chokonzedwa ndi bungwe loteteza zachilengedwe lotchedwa International Union for Conservation of Nature and Natural Resources.