Mawu a M'munsi
b Onani nkhani yakuti “Achinyamata Akufunsa Kuti . . . Kodi Ndichititse Opaleshoni Kuti Ndikhale Wokongola?” mu Galamukani! ya September 8, 2002. Komabe, munthu amene ali ndi matenda aakulu a maganizo angafunike kukaonana ndi dokotala wa maganizo.