Mawu a M'munsi
a Mtanthauzira mawu wina anati mayi woberekera mwana mayi wina ndi “mayi amene amakhala ndi pakati, nthaŵi zambiri poika ubwamuna m’thupi mwake kapena kuika dzira limene lasanduka mluza m’chiberekero mwake pomuchita opaleshoni, n’cholinga choti akhale ndi mimba yomwe mwana wake ndi wa mayi wina.”