Mawu a M'munsi
e Kuti mumve zambiri zokhudza mwamuna ndi mkazi okwatirana amene akufuna kupereka ubwamuna ndi dzira kuti aziphatikize kunja kwa thupi la mkaziyo kenako n’kuziika m’chiberekero chake, onani “Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga,” mu Nsanja ya Olonda yachingelezi ya June 1, 1981.