Mawu a M'munsi
b Malinga ndi kafukufuku wina amene anachitika ku United States, “anthu amene nthaŵi zambiri amamwa moŵa wambiri nthaŵi imodzi ndi amenenso kaŵirikaŵiri sapita ku sukulu masiku ena, sakhoza kusukulu, amavulazidwa, ndipo amawononga katundu, kuposa anthu amene samwa moŵa wambiri nthaŵi imodzi.”