Mawu a M'munsi
b Akristu odzipatulira amene akufuna kugwiritsa ntchito moyo wawo m’njira yovomerezeka pochita utumiki wopatulika kwa Mulungu, ali ndi zifukwa zowonjezereka zofunira kuchepetsa thupi n’kukhala athanzi. M’malo momwalira msanga, akhoza kugwiritsa ntchito moyo wawo kwa nthaŵi yaitali potumikira Mulungu.—Aroma 12:1.