Mawu a M'munsi
a Si anthu onse amene ali ndi kachilombo ka HIV amene amauzidwa kuti azimwa mankhwala ochepetsa mphamvu ya kachilomboka. Anthu amene ali ndi kachilombo ka HIV, kapena amene akuganiza kuti mwina angakhale nako, ayenera kukaonana ndi dokotala asanayambe kumwa mankhwala alionse. Magazini ya Galamukani! silangiza anthu kuti atsatire njira yakutiyakuti ya chithandizo.
[Chithunzi]
KU KENYA Dokotala akuphunzitsa wodwala Edzi za mankhwala ochepetsa mphamvu ya kachilombo ka HIV
[Mawu a Chithunzi]
© Sven Torfinn/Panos Pictures
[Chithunzi]
KU KENYA Wodwala Edzi akulandira mankhwala ake ochepetsa mphamvu ya kachilombo ka HIV kuchipatala
[Mawu a Chithunzi]
© Sven Torfinn/Panos Pictures